2 Akorinto 7:6 - Buku Lopatulika6 Koma Iye amene atonthoza odzichepetsa, ndiye Mulungu, anatitonthoza ife ndi kufika kwake kwa Tito; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Koma Iye amene atonthoza odzichepetsa, ndiye Mulungu, anatitonthoza ife ndi kufika kwake kwa Tito; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Koma Mulungu amene amalimbitsa otaya mtima, adatilimbitsa ndi kufika kwa Tito. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Koma Mulungu, amene amatonthoza mtima wopsinjika, anatitonthoza mtima ndi kufika kwa Tito, Onani mutuwo |