2 Akorinto 6:3 - Buku Lopatulika3 osapatsa chokhumudwitsa konse m'chinthu chilichonse, kuti utumikiwo usanenezedwe; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 osapatsa chokhumudwitsa konse m'chinthu chilichonse, kuti utumikiwo usanenezedwe; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Sitifuna kupatsa anthu chifukwa chonyozera ntchito yathu, nchifukwa chake sitikhumudwitsa munthu aliyense ndi kanthu kalikonse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Ife sitikuyika chokhumudwitsa pa njira ya wina aliyense, kuti utumiki wathu usanyozeke. Onani mutuwo |