2 Akorinto 5:8 - Buku Lopatulika8 koma tilimbika mtima, ndipo tikondwera makamaka kusakhala m'thupi, ndi kukhala kwathu kwa Ambuye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 koma tilimbika mtima, ndipo tikondwera makamaka kusakhala m'thupi, ndi kukhala kwathu kwa Ambuye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Ndithu tikulimba mtima, ndipo makamaka tikadakonda kutuluka m'thupi lathu lino ndi kukakhala kwa Ambuye. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Inde, ife tikulimba mtima, ndipo tikanakonda kulekana nalo thupi lathu ndi kukhala ndi Ambuye. Onani mutuwo |