2 Akorinto 5:7 - Buku Lopatulika7 (Pakuti tiyendayenda mwa chikhulupiriro si mwa chionekedwe); Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 (Pakuti tiyendayenda mwa chikhulupiriro si mwa chionekedwe); Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Pakuti timatsata chikhulupiriro, osati zopenya ndi maso. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Ife timakhala mwachikhulupiriro, osati mwa zooneka ndi maso. Onani mutuwo |