2 Akorinto 5:5 - Buku Lopatulika5 Ndipo wotikonzera ife ichi chimene, ndiye Mulungu, amene anatipatsa ife chikole cha Mzimu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ndipo wotikonzera ife ichi chimene, ndiye Mulungu, amene anatipatsa ife chikole cha Mzimu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Mulungu ndiye amene adatikonzeratu kuti tilandire zimenezi, ndipo adatipatsa Mzimu Woyera ngati chikole chake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Tsono ndi Mulungu amene anatikonzeratu ife kuti tilandire zimenezi. Iye anatipatsa Mzimu ngati chikole, kutsimikizira zimene zikubwera. Onani mutuwo |