2 Akorinto 5:13 - Buku Lopatulika13 Pakuti ngati tili oyaluka, titero kwa Mulungu; ngati tili a nzeru zathu, titero kwa inu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Pakuti ngati tili oyaluka, titero kwa Mulungu; ngati tili a nzeru zathu, titero kwa inu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Ngati tidachita ngati tapenga, tidachita zimenezi kuti tilemekeze Mulungu. Koma ngati tikuchita zanzeru, tikuchita zanzeru kuti tikuthandizeni. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Ngati ndife amisala, monga amanenera ena, nʼchifukwa chofuna kuti Mulungu alemekezedwe. Ngati si ife amisala, nʼkuti inu muthandizike. Onani mutuwo |