2 Akorinto 4:3 - Buku Lopatulika3 Koma ngatinso Uthenga Wabwino wathu uphimbika, uphimbika mwa iwo akutayika; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Koma ngatinso Uthenga Wabwino wathu uphimbika, uphimbika mwa iwo akutayika; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Koma ngakhale Uthenga Wabwino umene timalalika uli wophimbika, ngwophimbika kwa okhawo amene akutayika. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Koma ngakhale uthenga wathu wabwino utakhala wophimbika, ndi wophimbika kwa okhawo amene akutayika. Onani mutuwo |