2 Akorinto 3:4 - Buku Lopatulika4 Ndipo kulimbika kotere kwa Mulungu tili nako mwa Khristu: Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ndipo kulimbika kotere kwa Mulungu tili nako mwa Khristu: Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Mulungu akudziŵa kuti tikunena zimenezi chifukwa Khristu ndiye amatipatsa kulimba mtima kotere. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Kulimba mtima kumeneku tili nako pamaso pa Mulungu kudzera mwa Khristu. Onani mutuwo |