2 Akorinto 3:2 - Buku Lopatulika2 Inu ndinu kalata yathu, wolembedwa mu mitima yathu, wodziwika ndi wowerengedwa ndi anthu onse; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Inu ndinu kalata wathu, wolembedwa mu mitima yathu, wodziwika ndi wowerengedwa ndi anthu onse; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Kalata yotichitira umboniyo ndinu nomwe. Idalembedwa m'mitima mwathu, kuti anthu onse aidziŵe ndi kumaiŵerenga. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Inu ndinu kalata yathu, yolembedwa pa mitima yathu, yodziwika ndi yowerengedwa ndi aliyense. Onani mutuwo |