2 Akorinto 2:16 - Buku Lopatulika16 koma kwa ena fungo la moyo kumoyo. Ndipo azikwanira ndani izi? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 koma kwa ena fungo la moyo kumoyo. Ndipo azikwanira ndani izi? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Kwa amene akutayika, fungoli ndi la imfa, ndipo limaŵapha. Koma kwa amene akupulumuka, fungoli ndi la moyo, ndipo limaŵapatsa moyo. Nanga ndani angaithe ntchito yotere? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Kwa amene akuwonongeka ndife fungo la imfa, limawapha. Ndipo kwa amene akupulumuka ndife fungo lamoyo, limawapatsa moyo. Ndani angayithe ntchito yotereyi? Onani mutuwo |