2 Akorinto 2:11 - Buku Lopatulika11 kuti asatichenjerere Satana; pakuti sitikhala osadziwa machenjerero ake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 kuti asatichenjerere Satana; pakuti sitikhala osadziwa machenjerero ake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Cholinga chake nkuti Satana asatichenjerere, paja tikudziŵa njira zake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 kupewa kuti Satana angapezere mpata pa ife, pajatu timadziwa machenjerero ake. Onani mutuwo |