2 Akorinto 13:8 - Buku Lopatulika8 Pakuti sitikhoza kanthu pokana choonadi, koma povomereza choonadi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Pakuti sitikhoza kanthu pokana choonadi, koma povomereza choonadi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Pakuti sitingathe kuchita chilichonse chotsutsana ndi choona, koma zokhazokha zothandizira choonacho. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Pakuti sitingachite chilichonse chotsutsana ndi choonadi, koma chokhacho chovomerezana ndi choonadi. Onani mutuwo |