Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




2 Akorinto 13:12 - Buku Lopatulika

12 Mupatsane moni ndi kupsompsonana kopatulika.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

12 Mupatsane moni ndi chipsompsono chopatulika.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

12 Mupatsane moni mwa chikondi choona.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

12 Lonjeranani ndi mpsopsono wachiyero.

Onani mutuwo Koperani




2 Akorinto 13:12
5 Mawu Ofanana  

Ndipo ngati mupatsa moni abale anu okhaokha, muchitanji choposa ena? Kodi angakhale anthu akunja sachita chomwecho?


Mupatsane moni wina ndi mnzake ndi kupsompsonana kopatulika. Mipingo yonse ya Khristu ikupatsani moni.


Akupatsani moni abale onse. Mupatsane moni ndi kupsompsonana kopatulika.


Perekani moni kwa abale onse ndi chipsompsono chopatulika.


Mupatsane moni ndi kupsompsonana kwa chikondi. Mtendere ukhale ndi inu nonse muli mwa Khristu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa