2 Akorinto 13:1 - Buku Lopatulika1 Nthawi yachitatu iyi ndilinkudza kwa inu. Pakamwa pa mboni ziwiri kapena zitatu maneno onse adzakhazikika. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Nthawi yachitatu iyi ndilinkudza kwa inu. Pakamwa pa mboni ziwiri kapena zitatu maneno onse adzakhazikika. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Aka nkachitatu tsopano kuti ndibwere kwanuko. Mau a Mulungu akuti, “Mlandu uliwonse uzitsimikizika ndi umboni wa anthu aŵiri kapena atatu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Uwu ndi ulendo wachitatu ndikubwera kudzakuyenderani. “Nkhani itsimikizike ndi umboni wa anthu awiri kapena atatu.” Onani mutuwo |