2 Akorinto 12:16 - Buku Lopatulika16 Koma kukhale kotero; ine sindinalemetsa inu; koma pokhala wochenjera ine, ndinakugwirani ndi chinyengo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Koma kukhale kotero; ine sindinalemetsa inu; koma pokhala wochenjera ine, ndinakugwirani ndi chinyengo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Momwemo tsono, mudzandivomereza kuti ine sindidakhale ngati katundu wokulemetsani. Koma kapena wina adzati popeza kuti ndine wochenjera, ndidakuchenjeretsani. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Ena mwa inu amavomereza kuti sindinali cholemetsa. Komabe ena amaganiza kuti ndine wochenjera, ndipo ndinakuchenjererani. Onani mutuwo |