2 Akorinto 12:12 - Buku Lopatulika12 Zizindikirotu za mtumwi zinachitika pakati pa inu, m'chipiriro chonse, ndi zizindikiro, ndi zozizwa, ndi zamphamvu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Zizindikirotu za mtumwi zinachitika pakati pa inu, m'chipiriro chonse, ndi zizindikiro, ndi zozizwa, ndi zamphamvu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Ndidakutsimikizirani mopirira kwambiri kuti ndine mtumwi, pakuchita pakati panu zizindikiro, zozizwitsa ndi ntchito zina zamphamvu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Ndinapirira pokuonetserani zizindikiro za mtumwi weniweni, pochita pakati panu zizindikiro, zodabwitsa ndi ntchito zamphamvu. Onani mutuwo |