2 Akorinto 11:32 - Buku Lopatulika32 Mu Damasiko kazembe wa mfumu Areta analindizitsa mzinda wa Adamasiko kuti andigwire ine; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201432 M'Damasiko kazembe wa mfumu Areta analindizitsa mudzi wa Adamasiko kuti andigwire ine; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa32 Pamene ndinali ku Damasiko, bwanamkubwa woimirira mfumu Areta, adaaika alonda kuzinga mzinda wonsewo kuti andigwire. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero32 Ku Damasiko, bwanamkubwa woyimira Mfumu Areta, anayika alonda kuzungulira mzinda wonse kuti andigwire. Onani mutuwo |