2 Akorinto 11:33 - Buku Lopatulika33 ndipo mwa zenera, mudengu, ananditsitsa pakhoma, ndipo ndinapulumuka m'manja mwake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201433 ndipo mwa zenera, mudengu, ananditsitsa pakhoma, ndipo ndinapulumuka m'manja mwake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa33 Koma anthu adandiika m'dengu nanditsitsira pa windo la m'lingalo, motero ndidamthaŵira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero33 Koma abale anandiyika mʼdengu nanditsitsira pa chipupa kudzera pa zenera la mpandawo, motero ndinapulumuka mʼmanja mwake. Onani mutuwo |