2 Akorinto 11:24 - Buku Lopatulika24 Kwa Ayuda ndinalandira kasanu mikwingwirima makumi anai kuperewera umodzi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 Kwa Ayuda ndinalandira kasanu mikwingwirima makumi anai kuperewera umodzi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 Kasanu Ayuda adandikwapula mikwapulo 39. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 Andikwapulapo kasanu zikoti zija za Ayuda, makumi anayi kuchotsapo chimodzi. Onani mutuwo |