2 Akorinto 11:19 - Buku Lopatulika19 Pakuti mulolana nao opanda nzeru mokondwera, pokhala anzeru inu nokha. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Pakuti mulolana nao opanda nzeru mokondwera, pokhala anzeru inu nokha. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Inu mumati ndinu anzeru kwambiri, nchifukwa chake anthu opusa mumangoŵalekerera mokondwa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Inu mumalolera kukhala ndi zitsiru mokondwera chifukwa mumati ndinu anzeru! Onani mutuwo |