2 Akorinto 11:17 - Buku Lopatulika17 Chimene ndilankhula sindilankhula monga mwa Ambuye, koma monga wopanda nzeru, m'kulimbika kumene kwa kudzitamandira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Chimene ndilankhula sindilankhula monga mwa Ambuye, koma monga wopanda nzeru, m'kulimbika kumene kwa kudzitamandira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Zimene ndimati ndinena panozi si zimene Ambuye afuna kuti ndinene, koma ndikungonyada, monga momwe amachitira wopusa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Kudzinyadira kwangaku, sindikuyankhula monga mmene Ambuye akufunira koma ngati chitsiru. Onani mutuwo |