2 Akorinto 11:14 - Buku Lopatulika14 Ndipo kulibe kudabwa; pakuti Satana yemwe adzionetsa ngati mngelo wa kuunika. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Ndipo kulibe kudabwa; pakuti Satana yemwe adzionetsa ngati mngelo wa kuunika. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Zimenezitu si zododometsa ai, pakuti Satana yemwe amadzizimbaitsa, naoneka ngati mngelo wounikira anthu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Sizododometsa zimenezi, pakuti Satana mwini amadzizimbayitsa kuoneka ngati mngelo wowunikira anthu. Onani mutuwo |