2 Akorinto 10:3 - Buku Lopatulika3 Pakuti pakuyendayenda m'thupi, sitichita nkhondo monga mwa thupi, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Pakuti pakuyendayenda m'thupi, sitichita nkhondo monga mwa thupi, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Ndi zoona kuti ndife anthu, koma sitimenya nkhondo motsata za anthu chabe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Ngakhale ife timakhala mʼdziko lapansi, sitimenya nkhondo monga mmene dziko lapansi limachitira. Onani mutuwo |