2 Akorinto 1:10 - Buku Lopatulika10 amene anatilanditsa mu imfa yaikulu yotere, nadzalanditsa; amene timyembekezera kuti adzalanditsanso; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 amene anatilanditsa mu imfa yaikulu yotere, nadzalanditsa; amene timyembekezera kuti adzalanditsanso; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Ndiye amene adatipulumutsa ku zoopsa zotere za imfa, ndipo adzatipulumutsanso. Taika ndithu chikhulupiriro chathu pa Iyeyo choti adzatipulumutsanso. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Mulungu watilanditsa ku zoopsa zotere za imfa, ndipo adzatilanditsanso. Ife tayika chiyembekezo chathu pa Iyeyo kuti adzapitiriza kutilanditsabe. Onani mutuwo |