1 Yohane 5:2 - Buku Lopatulika2 Umo tizindikira kuti tikonda ana a Mulungu, pamene tikonda Mulungu, ndi kuchita malamulo ake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Umo tizindikira kuti tikonda ana a Mulungu, pamene tikonda Mulungu, ndi kuchita malamulo ake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Chodziŵira kuti timakonda ana a Mulungu nchakuti timakonda Mulungu ndi kutsata malamulo ake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Chodziwira kuti timakonda ana a Mulungu nʼchakuti timakonda Mulungu ndi kusunga malamulo ake. Onani mutuwo |