1 Yohane 3:3 - Buku Lopatulika3 Ndipo yense wakukhala nacho chiyembekezo ichi pa Iye, adziyeretsa yekha, monga Iyeyu ali Woyera. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndipo yense wakukhala nacho chiyembekezo ichi pa Iye, adziyeretsa yekha, monga Iyeyu ali Woyera. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Munthu aliyense amene ali ndi chiyembekezo chimenechi pa Khristu, amadzisandutsa woyera monga momwe Khristuyo ali woyera. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Aliyense amene ali ndi chiyembekezo ichi mwa Iye adziyeretse yekha, monga Iye ali woyera. Onani mutuwo |