1 Yohane 2:9 - Buku Lopatulika9 Iye amene anena kuti ali m'kuunika, namuda mbale wake, ali mumdima kufikira tsopano lino. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Iye amene anena kuti ali m'kuunika, namuda mbale wake, ali mumdima kufikira tsopano lino. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Munthu akamati ali m'kuŵala, komabe nkumadana ndi mnzake, akali mu mdima ameneyo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Aliyense amene amati ali mʼkuwunika, koma nʼkumadana ndi mʼbale wake ali mu mdima. Onani mutuwo |