1 Yohane 2:3 - Buku Lopatulika3 Ndipo umo tizindikira kuti tamzindikira Iye, ngati tisunga malamulo ake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndipo umo tizindikira kuti tamzindikira Iye, ngati tisunga malamulo ake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Pakutsata malamulo a Mulungu, ndi pamene tingatsimikize kuti timamdziŵa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Ife timatsimikiza kuti tikumudziwa ngati tikusunga malamulo ake. Onani mutuwo |