1 Samueli 9:5 - Buku Lopatulika5 Pamene anafika ku dziko la Zufu, Saulo anamuuza mnyamata amene anali naye, kuti, Tiye tibwerere; kuti atate wanga angaleke kusamalira abuluwo, ndi kutenga nkhawa chifukwa cha ife. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Pamene anafika ku dziko la Zufu, Saulo anamuuza mnyamata amene anali naye, kuti, Tiye tibwerere; kuti atate wanga angaleke kusamalira abuluwo, ndi kutenga nkhawa chifukwa cha ife. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Atafika ku dziko la Zufu, Saulo adauza mnyamata wake amene anali naye kuti, “Tiye tizibwerera, kuwopa kuti bambo wanga angaleke kusamala za abulu ndi kudera nkhaŵa za ife.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Atafika ku dera la Zufi, Sauli anawuza mnyamata wake kuti, “Tiye tibwerere, mwina abambo anga angasiye kudandaula za abulu ndipo adzayamba kudandaula za ife.” Onani mutuwo |