1 Samueli 8:18 - Buku Lopatulika18 Ndipo tsiku lija mudzafuula chifukwa cha mfumu yanu munadzisankhira nokha; koma Yehova sadzayankha inu tsiku lijalo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Ndipo tsiku lija mudzafuula chifukwa cha mfumu yanu munadzisankhira nokha; koma Yehova sadzayankha inu tsiku lijalo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Nthaŵi imeneyo ikadzafika, mudzalira komvetsa chisoni chifukwa cha mfumu imene mwadzisankhirayo, koma Chauta sadzakuyankhani.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Nthawi imeneyo ikadzafika inu mudzalira momvetsa chisoni chifukwa cha mfumu imene mwadzisankhira, koma Yehova sadzakuyankhani.” Onani mutuwo |