1 Samueli 7:8 - Buku Lopatulika8 Ndipo ana a Israele anati kwa Samuele, Musaleke kutipempherera kwa Yehova Mulungu wathu, kuti Iye atipulumutse m'manja a Afilistiwo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ndipo ana a Israele anati kwa Samuele, Musaleke kutipempherera kwa Yehova Mulungu wathu, kuti Iye atipulumutse m'manja a Afilistiwo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 ndipo adauza Samuele kuti, “Musaleke kutidandaulira kwa Chauta, Mulungu wathu, kuti atipulumutse kwa Afilistiŵa.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Choncho anati kwa Samueli, “Musasiye kutipempherera kwa Yehova Mulungu wathu, kuti atipulumutse mʼdzanja la Afilistiwa.” Onani mutuwo |