1 Samueli 7:4 - Buku Lopatulika4 Pomwepo ana a Israele anachotsa Abaala ndi Asitaroti, natumikira Yehova yekha. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Pomwepo ana a Israele anachotsa Abaala ndi Asitaroti, natumikira Yehova yekha. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Choncho Aisraele adachotsa Abaala ndi Aasitaroti, nayamba kutumikira Chauta yekha. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Choncho Aisraeli anachotsa milungu yawo ya Baala ndi Asitoreti ndi kutumikira Yehova yekha. Onani mutuwo |