1 Samueli 4:16 - Buku Lopatulika16 Ndipo munthuyo anati kwa Eli, Ine ndine amene ndachokera ku khamu la ankhondo, ndipo ndathawa lero ku khamu la ankhondo. Ndipo iye anati, Nkhondoyo idatani, mwana wanga? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Ndipo munthuyo anati kwa Eli, Ine ndine amene ndachokera ku khamu la ankhondo, ndipo ndathawa lero ku khamu la ankhondo. Ndipo iye anati, Nkhondoyo idatani, mwana wanga? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Munthuyo adauza Eli kuti, “Ine ndine amene ndachoka ku nkhondo. Ndathaŵa kumeneko lero lomwe.” Eli adamufunsa kuti, “Nanga nkhondo yayenda bwanji, mwana wanga?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Munthuyo anamuwuza Eli kuti, “Ine ndabwera kuchokera ku nkhondo, ndathawako lero lomwe lino.” Eli anafunsa, “Nanga nkhondo yayenda bwanji mwana wanga?” Onani mutuwo |