1 Samueli 4:10 - Buku Lopatulika10 Ndipo Afilisti anaponyana nao, nakantha Aisraele; iwowa nathawira, munthu yense ku hema wake; ndipo kunali kuwapha kwakukulu; popeza anafako Aisraele zikwi makumi atatu a oyenda pansi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndipo Afilisti anaponyana nao, nakantha Aisraele; iwowa nathawira, munthu yense ku hema wake; ndipo kunali kuwapha kwakukulu; popeza anafako Aisraele zikwi makumi atatu a oyenda pansi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Motero Afilisti adamenya nkhondo ndipo Aisraele adagonjetsedwa kotheratu, nathaŵira kwao. Nthaŵiyo kudaphedwa Aisraele okwanira 30,000, ankhondo oyenda pansi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Choncho Afilisti anamenya nkhondo, ndipo anagonjetsa Aisraeli. Iwo anathawa aliyense kwawo. Ankhondo a Aisraeli oyenda pansi okwanira 30,000 anaphedwa. Onani mutuwo |