Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




1 Samueli 30:5 - Buku Lopatulika

5 Ndipo akazi awiri a Davide anatengedwa ukapolo, Ahinowamu wa ku Yezireele ndi Abigaile mkazi wa Nabala wa ku Karimele.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Ndipo akazi awiri a Davide anatengedwa ukapolo, Ahinowamu wa ku Yezireele ndi Abigaile mkazi wa Nabala wa ku Karimele.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Nawonso akazi a Davide anali atatengedwa ukapolo. Maina ao anali Ahinowamu wa ku Yezireele ndi Abigaile mkazi wamasiye wa Nabala wa ku Karimele.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Akazi awiri a Davide, Ahinoamu wa ku Yezireeli ndi Abigayeli mkazi wa Nabala wa ku Karimeli anatengedwanso.

Onani mutuwo Koperani




1 Samueli 30:5
5 Mawu Ofanana  

Chomwecho Davide anakwera kunka kumeneko pamodzi ndi akazi ake awiri, ndiwo Ahinowamu Myezireele, ndi Abigaile mkazi wa Nabala wa ku Karimele.


Iyeyu anali nao akazi awiri; winayo dzina lake ndi Hana, mnzake dzina lake ndi Penina. Ndipo Penina anaona ana, koma Hana anali wouma.


Ndipo Davide anakhala ndi Akisi ku Gati, iye ndi anthu ake, munthu yense ndi a pabanja pake, inde Davide ndi akazi ake awiri, Ahinowamu wa ku Yezireele, ndi Abigaile wa ku Karimele, mkazi wa Nabala.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa