1 Samueli 30:29 - Buku Lopatulika29 ndi kwa iwo a ku Rakala, ndi kwa iwo a ku m'mizinda ya Ayerameele, ndi kwa iwo a m'mizinda ya Akeni; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201429 ndi kwa iwo a ku Rakala, ndi kwa iwo a ku m'midzi ya Ayerameele, ndi kwa iwo a m'midzi ya Akeni; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa29 a ku Rakala, a ku mizinda ya fuko la Ayeramiyele, a ku mizinda ya fuko la Akeni, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero29 Rakala, mizinda ya fuko la Ayerahimeeli, mizinda ya fuko la Akeni, Onani mutuwo |