1 Samueli 3:11 - Buku Lopatulika11 Ndipo Yehova ananena ndi Samuele, Taona, ndidzachita mwa Israele choliritsa mwini khutu kwa munthu yense wakuchimva. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Ndipo Yehova ananena ndi Samuele, Taona, ndidzachita mwa Israele choliritsa mwini khutu kwa munthu yense wakuchimva. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Tsono Chauta adauza Samuele kuti, “Tamvera, patsala pang'ono kuti ndichite chinthu mu Israele chimene chidzadabwitsa aliyense amene adzachimva. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Ndipo Yehova anati kwa Samueli, “Taona, patsala pangʼono kuti ndichite chinthu china mu Israeli chimene chidzadabwitsa aliyense amene adzamve. Onani mutuwo |