1 Samueli 28:3 - Buku Lopatulika3 M'menemo Samuele ndipo atafa, ndipo Aisraele onse atalira maliro ake, namuika mu Rama, m'mzinda mwao. Ndipo Saulo anachotsa m'dzikomo obwebweta onse, ndi aula onse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 M'menemo Samuele ndipo atafa, ndipo Aisraele onse atalira maliro ake, namuika m'Rama, m'mudzi mwao. Ndipo Saulo anachotsa m'dzikomo obwebweta onse, ndi aula onse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Nthaŵi imeneyi nkuti Samuele atafa, ndipo Aisraele atalira maliro ake, namuika ku mzinda wake ku Rama. Saulo anali atachotsa anthu onse olankhula ndi mizimu ndi anthu onse oombeza maula am'dzikomo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Nthawi imeneyi nʼkuti Samueli atamwalira, ndipo Aisraeli onse anamulira namuyika mʼmanda ku mzinda wake wa Rama. Sauli anali atachotsa mʼdzikomo anthu owombeza mawula ndi woyankhula ndi mizimu ya anthu akufa. Onani mutuwo |