1 Samueli 26:22 - Buku Lopatulika22 Davide nayankha, nati, Tapenyani mkondo wa mfumu! Abwere mnyamata wina kuutenga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Davide nayankha, nati, Tapenyani mkondo wa mfumu! Abwere mnyamata wina kuutenga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Apo Davide adayankha kuti, “Suwu mkondo wanu, mfumu. Tumani mmodzi mwa ankhondowo adzatenge. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Davide anayankha kuti, “Nawu mkondo wanu, mfumu. Tumani mmodzi wa anyamata anu abwere adzatenge. Onani mutuwo |