1 Samueli 26:18 - Buku Lopatulika18 Nati iye, Chifukwa ninji mbuye wanga amalondola mnyamata wake? Pakuti ndachitanji? Kapena m'dzanja langa muli choipa chotani? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Nati iye, Chifukwa ninji mbuye wanga amalondola mnyamata wake? Pakuti ndachitanji? Kapena m'dzanja langa muli choipa chotani? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Chifukwa chiyani mbuyanga mukundilondola ine mtumiki wanu? Kodi ndachita chiyani? Kodi tchimo langa nlotani? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Nʼchifukwa chiyani mbuye wanga mukundilonda ine mtumiki wanu? Kodi ine ndachita chiyani ndipo ndapezeka ndi cholakwa chotani? Onani mutuwo |