1 Samueli 25:9 - Buku Lopatulika9 Ndipo pakufika anyamata a Davide, analankhula ndi Nabala monga mau aja onse m'dzina la Davide, naleka. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndipo pakufika anyamata a Davide, analankhula ndi Nabala monga mau aja onse m'dzina la Davide, naleka. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Tsono anyamata a Davide aja atafika, adafotokozera Nabala zonse zimene Davide adaaŵauza. Ndipo iwowo adayembekeza. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Anyamata a Davide aja atafika, anamuwuza Nabala zonse zimene Davide anayankhula. Ndipo anadikira yankho. Onani mutuwo |