1 Samueli 25:41 - Buku Lopatulika41 Ndipo iye ananyamuka, nawerama nkhope yake pansi, nati, Onani, mdzakazi wanu ali kapolo wakusambitsa mapazi a anyamata a mbuye wanga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201441 Ndipo iye ananyamuka, nawerama nkhope yake pansi, nati, Onani, mdzakazi wanu ali kapolo wakusambitsa mapazi a anyamata a mbuye wanga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa41 Mkaziyo adagwada nagunditsa nkhope yake pansi, nati, “Ine mdzakazi wa mbuyanga Davide, ndili wokonzeka ngakhale kusambitsa mapazi a anyamata ake.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero41 Abigayeli anagwada nagunditsa nkhope yake pansi ndipo anati, “Ine mdzakazi wa mbuye wanga ndakonzeka kutumikira ngakhale kusambitsa mapazi a anyamata ake.” Onani mutuwo |