1 Samueli 25:40 - Buku Lopatulika40 Ndipo anyamata a Davide pakufika kwa Abigaile ku Karimele, analankhula naye, nati, Davide anatitumiza kwa inu, kukutengani, mukhale mkazi wake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201440 Ndipo anyamata a Davide pakufika kwa Abigaile ku Karimele, analankhula naye, nati, Davide anatitumiza kwa inu, kukutengani, mukhale mkazi wake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa40 Anyamata a Davide atafika kwa Abigaile ku Karimele, adamuuza kuti “Mfumu Davide watituma kuti tikutengeni, mukakhale mkazi wake.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero40 Anyamata a Davide atafika ku Karimeli anawuza Abigayeli kuti, “Davide watituma kwa iwe kuti tikutenge ukhale mkazi wake.” Onani mutuwo |
Ndipo pamene Davide anamva kuti Nabala adamwalira, iye anati, Alemekezedwe Yehova, amene anaweruza mlandu wa mtonzo wanga wochokera ku dzanja la Nabala, naletsa mnyamata wake pa choipa; ndipo Yehova anabwezera pamutu pa Nabala choipa chake. Ndipo Davide anatumiza wokamfunsira Abigaile, zakuti amtengere akhale mkazi wake.