1 Samueli 25:14 - Buku Lopatulika14 Koma mnyamata wina anauza Abigaile, mkazi wa Nabala, kuti, Onani, Davide anatumiza mithenga akuchokera kuchipululu kulonjera mbuye wathu; koma iye anawakalipira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Koma mnyamata wina anauza Abigaile, mkazi wa Nabala, kuti, Onani, Davide anatumiza mithenga akuchokera kuchipululu kulonjera mbuye wathu; koma iye anawakalipira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Tsono wanchito wina adauza Abigaile, mkazi wa Nabala, kuti, “Davide adatuma amithenga kuchokera ku chipululu kuti adzalonjere mbuyathu, koma iwo adaŵakalipira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Tsono mmodzi mwa antchito anawuza Abigayeli mkazi wa Nabala kuti, “Davide anatumiza amithenga kuchokera ku chipululu kudzalonjera mbuye wathu, koma iye anawalalatira. Onani mutuwo |