1 Samueli 24:9 - Buku Lopatulika9 Davide nanena ndi Saulo, Bwanji mulikusamalira mau a anthu akuti, Onani, Davide afuna kukuchitirani choipa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Davide nanena ndi Saulo, Bwanji mulikusamalira mau a anthu akuti, Onani, Davide afuna kukuchitirani choipa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Adafunsa Saulo kuti, “Chifukwa chiyani mumamvera mau a anthu amene amanena kuti, ‘Davide akufuna kukuphani?’ Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Anafunsa Sauli kuti, “Nʼchifukwa chiyani mumamvera mawu a anthu kuti, ‘Davide wakukonzerani chiwembu?’ Onani mutuwo |
Chifukwa chake mbuye wanga mfumu amvere mau a kapolo wake. Ngati ndi Yehova anakuutsirani inu kutsutsana ndi ine, alandire chopereka; koma ngati ndi ana a anthu, atembereredwe pamaso pa Yehova, pakuti anandipirikitsa lero kuti ndisalandireko cholowa cha Yehova, ndi kuti, Muka, utumikire milungu ina.