1 Samueli 24:8 - Buku Lopatulika8 Bwino lake Davide yemwe ananyamuka, natuluka m'phangamo, nafuulira Saulo, nati, Mbuye wanga, mfumu. Ndipo pakucheuka Saulo, Davide anaweramira nkhope yake pansi, namgwadira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Bwino lake Davide yemwe ananyamuka, natuluka m'phangamo, nafuulira Saulo, nati, Mbuye wanga, mfumu. Ndipo pakucheuka Saulo, Davide anaweramira nkhope yake pansi, namgwadira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Pambuyo pake Davide nayenso adatuluka m'phangamo, ndipo adaitana Saulo kuti, “Mbuyanga mfumu.” Saulo atacheuka, Davide adamgwadira pogunditsa nkhope yake pansi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Kenaka Davide anatuluka mʼphanga muja ndipo anayitana Sauli, “Mbuye wanga!” Sauli atayangʼana mʼmbuyo, Davide anawerama ndi kugunditsa nkhope yake pansi. Onani mutuwo |