1 Samueli 24:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo kunali, pakubwerera Saulo potsata Afilisti, anamuuza, kuti, Taonani, Davide ali ku chipululu cha Engedi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo kunali, pakubwerera Saulo potsata Afilisti, anamuuza, kuti, Taonani, Davide ali ku chipululu cha Engedi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Saulo atabwerako kumene ankamenyana ndi Afilisti kuja, adamva kuti Davide ali ku chipululu cha Engedi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Sauli atabwera kuchokera kumene amathamangitsa Afilisti anamva kuti, “Davide ali mʼchipululu cha Eni Gedi.” Onani mutuwo |