1 Samueli 23:29 - Buku Lopatulika29 Ndipo Davide anakwera kuchokera kumeneko, nakhala m'ngaka za Engedi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201429 Ndipo Davide anakwera kuchokera kumeneko, nakhala m'ngaka za Engedi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa29 Davide adachoka kumeneko, nakhala m'mapanga a ku Engedi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero29 Ndipo Davide anachoka kumeneko ndi kukakhala ku mapanga a ku Eni Gedi. Onani mutuwo |