1 Samueli 23:3 - Buku Lopatulika3 Ndipo anyamata a Davide ananena naye, Taonani, ife tikhalira m'mantha ku Yuda kuno; koposa kotani nanga tikafika ku Keila kuponyana ndi makamu a nkhondo a Afilisti. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndipo anyamata a Davide ananena naye, Taonani, ife tikhalira m'mantha ku Yuda kuno; koposa kotani nanga tikafika ku Keila kuponyana ndi makamu a nkhondo a Afilisti. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Koma Davide anthu ake adamuuza kuti, “Ngati tikuchita mantha ku Yuda konkuno, nanga nanji tikapita ku Keila kuti tikamenyane ndi magulu ankhondo a Afilisti? Kodi sitikaopa kwambiri kumeneko?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Koma anthu amene anali ndi Davide anati, “Ngati tikuchita mantha ku Yuda konkuno, nanji kupita ku Keila kukamenyana ndi ankhondo a Afilisti!” Onani mutuwo |