1 Samueli 23:11 - Buku Lopatulika11 Kodi amuna a ku Keila adzandipereka m'dzanja lake? Kodi Saulo adzatsikira ndithu, monga mnyamata wanu wamva? Yehova Mulungu wa Israele, ndikupemphani, muuze mnyamata wanu. Ndipo Yehova anati, Adzatsika. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Kodi amuna a ku Keila adzandipereka m'dzanja lake? Kodi Saulo adzatsikira ndithu, monga mnyamata wanu wamva? Yehova Mulungu wa Israele, ndikupemphani, muuze mnyamata wanu. Ndipo Yehova anati, Adzatsika. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Kodi anthu a ku Keila adzandipereka kwa Saulo? Kodi Saulo adzabweradi monga m'mene ine mtumiki wanu ndamvera? Inu Chauta, Mulungu wa Aisraele, ndikukupemphani kuti mundiwuze, ine mtumiki wanu.” Chauta adati, “Saulo abweradi.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Kodi anthu a Keila adzandipereka mʼmanja mwa Sauli? Kodi Sauli abweradi monga ndamvera ine mtumiki wanu? Inu Yehova Mulungu wa Israeli, chonde, ndiwuzeni ine mtumiki wanu.” Ndipo Yehova anati, “Sauli abweradi.” Onani mutuwo |